Mai Bertha Hanoki, ochokera m’boma la Nkhotakota amene akukhala pa msasa wa Ngala ngati malo omwe akukhala anthu omwe anakhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi, ati iwo sakufunanso kubwerera ku mudzi kwawo ku Kanthum’dende komwe anaona mavuto kamba ka kusefukira kwa madzi. Poyankhura ndi nyumba yolemba Nkhani ino, mayi Hanoki ati mudzi wa Kanthum’dende, mfumu yaikulu […]
The post Sitikufuna kubweleranso kwathu-atero mayi Hanoki appeared first on Malawi 24.