Sing’anga amangwidwa pobera mzimayi K125 000 atamunamiza kuti amachulukitsa ndalama

Ku Zomba, a Polisi amanga sing’anga wina waku Mozambique pomuganjizira kuti anabera mayi wina ponama kuti amachulukitsa ndalama. M’neneri wa polisi ya Zomba, a Patricia Sipiliano ati sing’angayu ndi a Asima Abdul a dera la Lichinga mdziko la Mozambique. A Sipiliano ati mayi wina, Linda Mfupika, anapita ku Chinamwali komwe anakumana ndi sing’angayu pa 3 […]

The post Sing’anga amangwidwa pobera mzimayi K125 000 atamunamiza kuti amachulukitsa ndalama appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください