Sindingasiye anthu anga akufa ndi Kolera ine kumakadyelera ku Ethiopia – Chakwera atuma nduna ku msonkhano wa AU

Ngati mumayesa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndi osalabadira a Malawi, mukuyenela kusintha maganizo. Ngati mumaona ngati mavuto akhuthukira pa dziko lino a Chakwera sakuwaona ndiye mwina mumangowalakwira. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera watuma nduna yake yoona za ma ubale a dziko lino ndi maiko ena a Nancy Tembo kuti akamuyimilire […]

The post Sindingasiye anthu anga akufa ndi Kolera ine kumakadyelera ku Ethiopia – Chakwera atuma nduna ku msonkhano wa AU appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください