Sindinati, ndisiya pokhapokha kayendetsedwe ka mpira kasinthe, watelo De Jongh

Mphunzitsi watimu ya Silver Strikers Pieter De Jongh yemwe akuoneka kuti alibe zoti kuno mkuchilendo wati ngati akuluakulu sasintha kayendetsedwe ka mpira wa miyendo mdziko muno, iye apitilirabe kudzudzula pazolakwika zonse zomwe akuziona. De Jongh yemwe anafika mdziko muno kumayambiliro kwa chaka chino kudzaphuzitsa timu ya Silver Strikers wati zinthu zambiri ndizofunika zitasinthidwa m’masewero a […]

The post Sindinati, ndisiya pokhapokha kayendetsedwe ka mpira kasinthe, watelo De Jongh appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください