M’modzi mwa omwe akufuna kudzaimila kudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wa dziko lino kudzela ku chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) a Dalitso Kabambe ati iwo alibe maganizo aliwonse ogwirizana ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera monga akumvekera manong’onong’o kuti akufuna kudzayenda limodzi mu masankho a 2025. Poyankhula mu uthenga wawo wa Chaka […]
The post Sindinakumaneko ndi a Chakwera – Kabambe appeared first on Malawi 24.