..wadzudzula a polisi ya Kanengo pomunena kuti anasiya upolisi kuti adziba Shoveli wa thilaki yemwe akuzemba unyolo, Grey Chisinga, wakanitsitsa kuti iye anaba ndikugulitsa feteleza yemwe adanyamula komanso wati sanalande wa polisi mfuti koma kuti wapolisiyo anayisiya mfutiyo pansi zomwe zinamupatsa mwayi kuti ayitenge ndikuombera m’mwamba. Apolisi munzinda wa Lilongwe akusaka a Chisinga powaganizira kuti […]
The post Sindinabe feteleza, sindinalande wa polisi mfuti – oyendetsa thilaki Grey Chisinga wakanitsitsa appeared first on Malawi 24.