Sikuli bwino uku! a Kachaje ati mafuta ayambanso kusowa

Uja amatamika ndi za mafuta ngambwi ngambwi ali kuti? Chifukwa tsopano akuyenera kupepesa a Malawi, azingoyenda ali werawera. Mkulu wa bungwe la MERA a Henry Kachaje ati za mafuta ngambwi ngambwi ndi zoduka mutu, posachedwapa tionanso mizere ija. Polankhula ku bungwe loyang’anira za mphamvu ndi kusintha kwa nyengo la nyumba ya malamulo, a Kachaje ati […]

The post Sikuli bwino uku! a Kachaje ati mafuta ayambanso kusowa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください