Zakaliya (Kumanja) kuyankhula ndi a Chakwera Mlimi wa fodya yemwe anafusa mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera fuso lothina, wakana kuti wamenyedwa ndi apolisi. Izi zikutsatira makanema awiri amene anthu akugawana mmasamba anchezo omwe anajambulidwa lero pomwe mtsogoleri wadziko lino amakatsekulira malonda afodya mumzinda wa Lilongwe. Kanema oyamba akusonyeza mlimiyu Msaiwale Zakaliya wina akuyankhulana ndi a […]
The post Si ine – mlimi ofusa Chakwera wakana kuti wapandidwa appeared first on Malawi24.