M’modzi mwa anthu oyimba mdziko muno Shammah Vocals wapempha mipingo kuti ikhale patsogolo yochititsa misonkhano ya achinyamata kuti idziwalimbikitsa zatsogolo labwino la moyo wao. Shammah Vocals yemwe dzina lake leni leni ndi Shammah Sitola wayankhula izi ndi Malawi24 ku Malindi Secondary School ku Zomba pomwe adakayimba ndikusangalatsa achinyamata pa nsonkhano wamapemphero omwe udachititsa ndi mpingo […]
The post Shammah Vocals wati mipingo ikhale patsogolo yolimbikitsa achinyamata zatsogolo labwino appeared first on Malawi 24.