Pamene anthu m’dziko muno akuchita nthabwala ndi kuchuluka kwa mbatata ya kholowa yomwe siyinasiye malo, katswiri wina wa zaulimi walangiza anthu komaso alimi kuti asamale kwambiri chakudyachi. Kwa ka nthawi tsopano, anthu ochuluka m’dziko muno makamaka m’masamba a nchezo, akukambilana za mpweche wa mbatata omwe dziko la Malawi ladalitsika nawo. Ena akunyogodola kuchuluka kwa mbatatazi […]
The post Samalani mbatatayo ndi dilu – watelo katswiri wa zaulimi appeared first on Malawi24.