Samalani chakudya, kuli njala- Joyce Banda

Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Joyce Banda, walangiza mzika za dziko lino kusamala chimanga kamba ka njala yoopsa yomwe iyale mphasa chaka chino chifukwa cha kusintha kwa nyengo. A Banda ayankhula izi Lachitatu ku Domasi komwe  amapereka chakudya, zikwama komaso kukhazikitsa ntchito yokonzanso zinthu zina ndi zina pa Gala pulayimale sukulu ndipo ati pakufunika machawi […]

The post Samalani chakudya, kuli njala- Joyce Banda appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください