Ogwira ntchito za pakhomo komanso m’mashopu ati ndi chitonzo chachikulu chomwe boma lapanga chifukwa iwowa amagwira ntchito yambiri ndipo ati n’zomvetsa chisoni kuona boma likufananiza malipiro awo ndi thumba limodzi la chimanga. Izi ogwira nthitowa anena mu mzinda wa Lilongwe pomwe anachititsa msonkhano wa atolankhani poonetsa kusakondwa ndi ganizo la boma pa malipiro a anthu […]
The post Salary K52000 thumba lachimanga K50 000? Adabwa ogwira ntchito zapakhomo pokana zomwe boma lakhazikitsa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.