Bungwe la Malawi Red Cross Society lati lidzipereka kuthandiza anthu omwe akhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi mu chigawo chapakati ndi kumpoto kwa dziko lino chifukwa ndipo lati chiwerengero cha anthu omwe akusowekera thandizo ndi malo okhala ndi chochuluka. Mkulu oyang’anira zochitikita ndi chitukuko cha anthu mu bungweli, Prisca Chisale, ndiye anayankhula izi pamene amagawa zipangizo […]
The post Red Cross yati ipitiriza kufikira anthu omwe akhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 