RBM yati ithana ndi  amalonda amene amakana ndalama zina ponena kuti zidatha mphamvu

Reserve Bank of Malawi (RBM), yomwe ndi banki yayikulu m’dziko muno, yachenjeza kuti ithana ndi aliyense amene apezeke akukana ndalama ponena kuti inatha mphamvu ndipo potsindika za nkhaniyi a RBM ati ngakhale ma 1 tambala ndi ovomerezeka kugulira chinthu. Malingana ndi mneneri wa bankiyi, Dr Mark Lungu wati a Malawi akuyenera azipanga lipoti munthu amene […]

The post RBM yati ithana ndi  amalonda amene amakana ndalama zina ponena kuti zidatha mphamvu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください