Ralph Mhone , Mganda Chiumia ndi Welani Chilenga alowa MCP

Mphekesera zikumveka kuti a Ralph Mhone , Mganda Chiumia ndi Welani Chilenga alowa chipani cha Malawi Congress (MCP). Ena omwe mphekesera zikusonyeza kuti alowa MCP ndi katswiri odziwa kuyimba nyimbo zanthetemya zochemerera chipani a Miriam Chimbalanga. Malingana ndi malipoti omwe matsamba ena atsindikiza, anthuwa alandilidwa ndi chipani pompano. Chipani cha MCP chakhala chikulandila anthu ambiri […]

The post Ralph Mhone , Mganda Chiumia ndi Welani Chilenga alowa MCP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください