Pulofeti wina kwa Jenda ali m’manja mwa apolisi kamba kogwililira mkazi wamwini yemwe anapita ku tchalitchi cha mneneriyu kuti akamupempherere pa vuto lakusowa mphatso ya mwana m’banja. Mayiyu yemwe wakhala miyezi itatu m’banja koma osatenga pakati, anaganiza zopita ku tchalitchi cha mneneriyu kuti akamupempherere kamba kavutoli. Chodabwitsa mchakuti mayiyu atafika ku tchalitchi cha mneneriyu yemwe […]
The post Pulofeti wanjatidwa kamba kogwililira mkazi wamwini appeared first on Malawi 24.