Pulofeti ochita za akuluakulu ndi mwana wake uja wagamulidwa zaka 19

Mneneri Christopher Phiri wa zaka 40 yemwe ndi mwini utumiki wa Supernatural Embassy ku Mangochi, wagamulidwa kukaseweza jere zaka khumi, mphambu zisanu ndi zinayi (19) kamba koseweretsa malo obisika a mwana wawo wa mkazi wa zaka 16 zomwe akuti zinali ndi kuthekera koti anakatha kugonana naye. Ngakhale Phiri aloza chala mwana wawoyo kuti anachita kuwaputa […]

The post Pulofeti ochita za akuluakulu ndi mwana wake uja wagamulidwa zaka 19 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください