Yemwe adayambitsa mpingo wa Life International Church, Prophet Amos Kambale, walangiza boma la a President Lazarus Chakwera kuti lileke kudalira thandizo lochokera mayiko akunja, koma kuti lipeze njira zomwe zingathandize potukula chuma cha dziko lino. A Kambale adanena izi mu ulaliki wawo wolowera chaka chatsopano cha 2024. Mpingowu udakonza mapemphero antchezero pa sukulu ya Mbinzi […]
The post Pulofeti awuza a Chakwera zofunika kuchita kuti chuma cha Malawi chiyende appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.