Professor Ngeyi Kanyongolo awasankha kukhala wachiwiri kwa wamkulu wa Catholic University

Bungwe la mabishopu achikatolika la Episcopal Conference of Malawi (ECM) lasankha katswiri pankhani ya zamalamulo Professor Ngeyi Kanyongolo kukhala wachiwiri kwa wamkulu wa Catholic University. Bungwe la ECM lalengeza zakusankhidwa kwa a Kanyongolo kudzera muchikalata chomwe bungweli latulutsa. Chikalatachi chomwe wasayinira ndi wapampando wa bungwe la ECM Archbishop George Desmond Tambala chati asankha Prof Kanyongolo […]

The post Professor Ngeyi Kanyongolo awasankha kukhala wachiwiri kwa wamkulu wa Catholic University appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください