PrEP wobaya oteteza kutenga HIV akupelekedwa ku Blantyre, Lilongwe

Pali chiyembekezo choti chiwerengero cha anthu otenga kachilombo ka HIV chitha kuchepa mdziko muno kamba koti unduna wa zaumoyo walengeza kuti PrEP wobaya yemwe amathandiza kuchepetsa chiopsyezo chotenga kachilombo ka HIV, wayamba kupelekedwa mzipatala zina ku Lilongwe komaso Blantyre. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe undunawu watulutsa Lamulungu pa 24 March, 2024 yomwe wasainira ndi […]

The post PrEP wobaya oteteza kutenga HIV akupelekedwa ku Blantyre, Lilongwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください