Mchaka cha 2013 maiko ndi bungwe onse amene amathandiza dziko lino adalengeza kuti asiya kuthandiza dziko lino kamba ka ziphuphu ndi katangale zomwe zinkachitika nthawi imeneyo. Atangolowa mboma , onse anabwerelera nkuyambanso kuthandiza dziko lino. Ichi nchifukwa chake Nduna yazachuma a Simplex Chithyola Banda yati anthu oposa 570,000 omwe adakhudzika ndi mavuto akusintha kwa nyengo […]
The post appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.