‘Ponya kaye K10,000 mami, onetsa lavu’ – mneneri Habakkuk watekesa pa intaneti

…akuti ku utumiki kwawo aziyimba nyimbo za hipapa, piyano Aneneri ndi onse koma umanena uyo wakulasa mtima mosayang’anira maonekedwe, ndipo poti dzuwa salozerana, sizochitaso kukambirana kuti mneneri Habakkuk watenga mitima ya mazana mazana ya aMalawi. Timutche mneneri wa pa intaneti? Masiku ano ukumati ukalowa m’masamba anchezo, mwa zinthu khumi zoyambilira kuziona, zisanu ndi ziwiri zikumatha […]

The post ‘Ponya kaye K10,000 mami, onetsa lavu’ – mneneri Habakkuk watekesa pa intaneti appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください