Akayidi okwana 48 tsopano akhala akusimba lokoma kutsatira mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wakhululukira ndikumasula akayidiwa mnyengo ino yachikondwerero cha khilisimasi komanso chaka chatsopano. Malingana ndi chikalata chomwe atulutsa a Oliver Kumbambe yemwe ndi mlembi wamkulu muunduna wazachitetezo, mtsogoleri wa dziko lino wakhululukira akayidiwa omwe tsopano agwira theka lazaka zomwe khothi lidawagamula. Mwa akayidi […]
The post Pitani ndakukhululukirani koma musakachimwenso: Chakwera wakhululukira akaidi appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 