Phungu wa Zomba Malosa wagona ku ma ofesi a Works Training Center kufuna chimanga

Phungu wa mdera la Zomba Malosa Grace Kwelepeta wagona kuma ofesi a Zomba Training Center kufuna kukakamiza galimoto yayikulu  yomwe yanyamula chimanga chogawira anthu mwaulele omwe akuvutika ndi njala kuti ipite mdera lake. Kwelepeta wauza Malawi24 kuti chiyambireni Boma kugawira anthu chimanga mu mwezi wa October chaka chatha anthu a mdera lake alandira kamodzi kokha […]

The post Phungu wa Zomba Malosa wagona ku ma ofesi a Works Training Center kufuna chimanga appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください