Phungu wa Chikwawa West a Susan Dossi, yemwe anawina ngati phungu oyima payekha kenako nkulowa UTM, wati chipanichi sichinamufikire ndi uthenga woti achoke ku mbali ya boma kupita yotsutsa boma. A Dossi ati ngakhale chipanichi chitawafikira, sakuona phindu lochoka mbali ya boma chifukwa anthu kudera lawo akufuna chitukuko chomwe chimachokanso kuboma komweko. “Kodi nkachoka ku […]
The post Phungu wa UTM Susan Dosi akuti: “Kodi nkachoka ku boma kupita ku opposition, zipindulira ndani?” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.