Phungu wa chipani cha Democratic Progressive Party wa dera la kumpoto m’boma la Mangochi, Benedicto Chambo, wati agwira ntchito yothandiza kuti mu 2025, President Lazarus Chakwera apitirize kulamula dziko lino. Phunguyu lero adali nawo pa msonkhano wa chipani cha Malawi Congress umene unachitikira pa bwalo la masewero la Dzenza, ku Area 25 m’boma la Lilongwe. […]
The post Phungu wa DPP ku Mangochi wati awonesesa kuti Chakwera apitilize kuyendesa Malawi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.