Phungu wa DPP a Suleman akufuna mkulu wa Immigration atule pansi udindo

Phungu wa nyumba ya malamulo wa Blantyre South East  Sameer Suleman wati m’kulu wa Nthambi yoona za anthu otuluka ndi kulowa m’dziko muno (immigration) atule pansi udindo kamba koti palibe chomwe akuchita ndipo wakalamba. A Suleman ati nzokhumudwitsa kuti mpaka pano ziphaso zoyendera sizikupangidwa zomwe zikusokoneza ntchito za a  Malawi ambiri. Iwo ati izi zikuchitika […]

The post Phungu wa DPP a Suleman akufuna mkulu wa Immigration atule pansi udindo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください