Phungu opuma azilandira ndalama moyo wawo onse – watelo Chilenga

Pamene dziko lino likuvutika pa nkhani ya zachuma, phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kum’mwera kwa boma la Chitipa a Werani Chilenga, ati akufuna kuti nyumba ya malamulo ikambirane zoti aphungu opuma azilandira malipiro a pamwezi kwa moyo wawo onse. Izi ndi malingana ndi chikalata cha a Chilenga chomwe chikuzungulira m’masamba a mchezo […]

The post Phungu opuma azilandira ndalama moyo wawo onse – watelo Chilenga appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください