Nyimbo yake mwina nkukhala ya “timalizeni, tatsala pati?” kapena mwina ija ya pa mauthenga a chisoni ya “Atimwe”. Banki yaikulu ya mu dziko muno yaswa nkhonya ina yowawa: Malawi Kwacha yagwanso. Malinga ndi chikalata chimene bankiyi yatulutsa, iwo ati pa malonda a msinthano amene anachititsa zaoneka kuti Kwacha tsopano yagwa ndi 3 Kwacha pa 100 […]
The post Phi!! Yagwanso Malawi Kwacha appeared first on Malawi 24.