Gule kwawo: dela la mfumu yayikulu Chimutu ku Lilongwe, laletsa vilombovi kumapemphetsa m’misewu komaso kupezeka m’masukulu ndi m’misika, ndipo ati zikapezeka zikuchita izi zidzigwidwa ndi kukasiyidwa ku polisi. Izi zili mu chikalata chomwe dela la mfumu yayikulu Chimutu latulutsa chodziwitsa anthu komaso akuluakulu a madambwe za malamulo atsopanowa ndipo chikalatachi chasayinidwa ndi mafumu asanu (5), […]
The post Pezani zina zochita; gule wamkulu opemphetsa waletsedwa kwa Chimutu appeared first on Malawi24.