Pemphero Mphande ndi ine tili pa ubwezi – watsindika Keturah

Mtsikana odziwika ndi luso lokalasa nsambo komanso kuimba chamba cha Afro-Pop kuno ku Malawi, Keturah, watsimikizira onse omutsatira kuti iye ali pa ubwenzi ndi Pemphero Mphande. Mu uthenga wake kudzera mu kanema ozijambula yekha yemwe wapereka kwa onse omutsata pa omutsatira lake la mchezo la Facebook mu usiku wa pa 20 April 2022, mtsikanayu anati […]

The post Pemphero Mphande ndi ine tili pa ubwezi – watsindika Keturah appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です