Pamene mafuta agalimoto akupitilira kusowa m’dziko muno, bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lati anthu onyamula zigubu asaloledwe kugula mafuta pamalo omwetsera mafuta. Mu chikalata chomwe yatulutsa, MERA yati anthu ena akumagula mafuta ambili mu zigubu ndi cholinga chokuti akagulitsenso mafutawo pa mtengo okwera zomwe zikupangitsa kuti mafuta azipitilira kusowa. Malingana ndi bungweli, kugulitsa […]
The post Pasapekeze ogulitsa mafuta mu zigubu — yatero MERA appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 