Papa wati mpingo wakatolika uzidalitsa maukwati a amuna kapena akazi okhaokha

Papa Francis waloleza mpingo wa Katolika pa dziko lonse, kuphatikizapo kuno ku Malawi, kuti uzidalitsa maukwati a amuna kapena akazi okhaokha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe yatulutsa ofesi yoona za malamulo oyendetsera mpingo ku Vatican. Papa yemwe ndi mkulu wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse wati ansembe asakanize Kapena kulepheretsa anthu kukhala chifupi […]

The post Papa wati mpingo wakatolika uzidalitsa maukwati a amuna kapena akazi okhaokha appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください