Amafuna kutulukira pawindo koma abwalo akamumbwandira. Mulandu wake wa katangale upitilira basi, ndipo akapezeka olakwa Batatawala n’kutheka akasewenza jele. Oganiziridwa pa milandu ingapo ya katangale, a Abdul Karim Batatawala achoka ndi nkhope ya manyazi ku bwalo la milandu dzulo pamene a bwalo alamula kuti mulandu wawo umodzi pa ingapo okhudza katangale upitilirebe. A Batatawala amene […]
The post Palibe kuthawa apa – a bwalo ampanilira Batatawala appeared first on Malawi 24.