Palibe kothawira, nayo kampani ya Salima Sugar yakweza mtengo wa shuga wake

Kokapumira ndi kumwamba basi. Patangotha ma ola bungwe la Blantyre Water Board litalengeza kuti lakweza madzi ndinso kampani ya Illovo italengeza kuti shuga wake yakweza, nayo kampani ya Salima Sugar yalowa m’bwalo pofuna kuonetsetsa kuti anthu asamwenso thiyi basi. Akweza sugar wawo. Malinga ndi kampaniyi, iwo ati shuga wawo amene amagulitsa pa mtengo wa MK1900 […]

The post Palibe kothawira, nayo kampani ya Salima Sugar yakweza mtengo wa shuga wake appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください