Prophet Shepherd Bushiri wati pakali pano ntchito yawo yogawa chimanga chaulere kwa a Malawi omwe akhuzidwa ndi ngozi zadzidzidzi yikupitilirabe ndipo panopa afikira anthu oposa 700 000. Mneneri wa a Bushiri a Aubrey Kusakala anena izi ku Mangochi komwe athandiza mabanja oposa 200 mdera la Senior Chief Nankumba ku Monkey-Bay m’boma la Mangochi. A Bushiri […]
The post Pakali pano tafikira anthu oposa 700 000 ndi chimanga chaulere, atero Bushiri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.