Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, apemphedwa ndi Bungwe lotchedwa Public Affairs Committee (PAC) kuti achepetse nduna zake komanso chiwerengero cha azilangi ake ndicholinga chofuna kupulumutsa chuma pamene dziko lino lakutidwa ndi mavuto osiyanasiyana azachuma. Bungwe la atsogoleri a mipingowa linaykuonongeka mdziko muno kamba kakuti mtsogoleri wadziko linoyu amachita ziganizo mochedwa komanso sakhazikika muzochitika […]
The post PAC yapempha a Chakwera kuti achepetse chiwerengero cha nduna komanso alangizi appeared first on Malawi 24.