Oyimba hipapu ambiri akumveka ngati Gwamba – watero Dominant 1

…wati nyimbo zambiri ku Malawi ndi mbwelera Oyimba nyimbo zogwira palisani, hipapu (hiphop), Dominant 1 wabweretsa chifwilimbwiti pa masamba amchezo pomwe wang’alura oyimba anzake kuti ambiri akubera mmene amaimbira Gwamba ndipo wati nyimbo zambiri ku mpanje kuno ndi panja penipeni. Nkhaniyi yayamba kumayambiliro kwa sabata yatha pomwe Dominant 1 yemwe pano a kukhala m’dziko la […]

The post Oyimba hipapu ambiri akumveka ngati Gwamba – watero Dominant 1 appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください