Osataya tsache lakale: Chakwera atuma Bakili Muluzi ku maliro

Yemwe adati chikuni chachikulu chimasunga moto adalinga ataona kaamba koti mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wasankha mtsogoleri wakale a Bakili Muluzi kukawaimilira ku maliro a mtsogoleri wakale wa dziko la Zambia a Rupiah Bwezani Banda. A Banda omwe anali ndi zaka 85, amwalira Lachisanu sabata yatha pa 11 March ndipo thupi lawo likuyembekezeka […]

The post Osataya tsache lakale: Chakwera atuma Bakili Muluzi ku maliro appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です