Kunali nkhanza pamene apolisi anapita kukagwila Mayi Martha Chizuma, Malawi24 yapeza choncho. Kupatula kuwakwenyakwenya, ati apolisi amauza a Chizuma kuti asamayankhule nawo chiyimile. Pa malipoti amene ayalidwa mu nyumba ya malamulo ndi a Kondwani Nankhumwa, ati apolisi anachita ndi Mayi Chizuma monga akuchita ndi chigandanga choopsa. Mwa zina, ati apolisi analetsa Mayi Chizuma kukatenga Magalasi […]
The post Osamayankhula ndi boma utaima, gwada…apolisi anapinditsa maondo Mayi Chizuma appeared first on Malawi24.