Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, a Saulos Chilima, ati a Malawi asiye kuliopseza boma ndi mavoti awo. Iwo anena izi ati ngati munthu wamba pothirapo ndemanga pa mkumano wa bungwe la anthu otsata zachuma la Economists Association of Malawi (ECAMA) ku Mangochi. A Chilima amene ali mu boma la mgwirizano ndi a Chakwera ati […]
The post Osamatiopseza ndi mavoti anu – Chilima appeared first on Malawi 24.