Osamatengeka ngati mwana wa zaka ziwiri akaona chimsope — Chilima auza a Gotani Hara

Wachiwili kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima wasambwaza sipika wa nyumba ya malamulo a Gotani Hara ati kamba kosokoneza mgwilizano wa pakati pa Kongeresi ndi UTM. Polankhula lachisanu pamene amalankhula kwa owatsatila komanso a Malawi malinga pamene anatchulidwa kuti ndi katswiri wa katangale, a Chilima anati anthu ena mu mgwilizano wa Tonse akomedwa […]

The post Osamatengeka ngati mwana wa zaka ziwiri akaona chimsope — Chilima auza a Gotani Hara appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です