Osamadikula mu tchalichi mukamavina — Bishopu wachenjeza a Katolika

A Katolika awachenjeza kuti asamadikule mu tchalichi chifukwa kavinidwe kotero kangathe kupangitsa kuti akhristu anzawo achimwe. Bishopu wa ku Ndola a Benjamin Phiri ati ndi okhudzidwa ndi m’mene anthu amavinila mu tchalichi pa nthawi ya Misa popeza ena amadikula kwambiri. Malingana ndi mkulu wa ansembeyu yemwe mawu ake asindikizidwa ndi nyuzipepala ya Ku Zambia ya […]

The post Osamadikula mu tchalichi mukamavina — Bishopu wachenjeza a Katolika appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください