Ophunzira wa sitandade 5 wadzipha atamuletsa kuchita zibwezi

Ophunzira wamkazi wa sitandade 5 ku Mulanje wadzipha chifukwa chokwiya ndi malangizo amayi ake omuletsa khalidwe lake lopanga zibwenzi atadziwa kuti akuchita chibwezi ndi m’nyamata wina mdelaro. Nkhani yonse ikuti mtsikanayu, yemwe dzina lake ndi Eneles Namusanyo ndipo ndi wazaka 15 zakubadwa anali pa ubwezi ndi m’nyamata wina. Amayi ake atamva za nkhaniyi anaganiza zokhala […]

The post Ophunzira wa sitandade 5 wadzipha atamuletsa kuchita zibwezi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください