Ophunzira pa Ntcheu Sekondale atopa ndi chakudya chowawa

Pena munthu umafikadi potopa ngati momwe atopera ophunzira pa sukulu ya boma ya Ntcheu sekondale omwe adandaula kuti chitsekulireni sukuluyi mwezi watha, akupatsidwa chakudya chowawa kwambiri. Izi zadziwika lero la chiwiri pa 10 October pomwe ophunzirawa anatengana onse ndikupita ku ofesi ya mkulu wa za maphunziro m’bomali kukatula madandaulo awo okhudza chakudya chomwe akupatsidwa. Ena […]

The post Ophunzira pa Ntcheu Sekondale atopa ndi chakudya chowawa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください