Ophunzira apa sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu University (Mzuni) awauza kuti abwerele ku sukulu Lolemba pa 23 October. Izi zadza kutsatira chikalata chomwe sukuluyi yatulutsa mmawa wa lero. Sukuluyi yakana kutsitsa mitengo ya tsopano ya fizi yomwe idapangitsa kuti ophunzirawa achite zionetsero pofuna kuti mitengoyi itsike ndikuti mitengo yatsopanoyi idzayambe kugwira ntchito akamadzayamba chaka chatsopano. […]
The post Ophunzira ku Mzuni abwelera kusuluku sabata lamawa appeared first on Malawi 24.