Ophunzira a Sukulu ya sekondale ya Balaka achoka pasukulu

Ophunzira pa sukulu ya sekondale yogonera konko ya Balaka achoka pa sukulupa ndipo ena afika kale m’makwawo ati kaamba ka kusakhutitsidwa ndi zakudya zomwe amapatsidwa pasukuluyi. Malawi24 yamvetsedwa kuti ana ena afika m’makwawo m’bandakucha wa tsiku lalero lamulungu. Poyankhula ndi Mtolankhani wathu, ophunzira ena amene tinawapeza akungozungulira mu tawuni ya Balaka ati atopa  ndi kudya […]

The post Ophunzira a Sukulu ya sekondale ya Balaka achoka pasukulu appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy