Bungwe la National Advocacy Platform ladzudzula khalidwe lotchingira ndi kugenda galimoto za pamdipiti wamtsogoleri wa dziko lino ponena kuti simoyo wabwino ndipo onse okhudzidwa pa mchitidwewu akuyenera kuzengedwa Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa ndipo wasayinila ndi wapampando wabungweli a Benedicto Kondowe, yati mchitidwewu ndi oyipa kaamba kakuti izi zimayika pachiopsezo chitetezo cha mtsogoleri wadziko […]
The post Onse omwe adayimitsa galimoto zapam’dipiti wa a Chakwera afufuzidwe, yatero NAP appeared first on Malawi 24.