Ngati njira imodzi yochepetsera mavuto omwe anthu omwe anakhuzidwa ndi namondwe wa Freddy akukumana nawo, bungwe la Child Focus likulimbikitsa anthu okhala m’mudzi wa Sambazi, mfumu yaikulu Phimbi m’boma la Balaka kuchita ulimi wamthilira. Monga mmene zidakhalira mmadera ena a mchigawo cha kummwera kwa dziko la Malawi, namondwe wa Freddy adawononga katundu osiyanasiyana monga nyumba,misewu […]
The post Okhudzidwa ndi Namondwe Freddy alimbikitsidwa kuchita ulimi wamthilira appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 
