Ogwira ntchito zaumoyo awopsyezaso kutengera unduna ku khothi

Gulu la anthu ogwira ntchito zaumoyo omwe sanalembedwebe ntchito, awopseza kuti apitilira ndi ganizo lawo lokasumira unduna wa zaumoyo pa zotsamwitsa zomwe zinachitika pa ndondomeko yolemba anthu ntchito ngati undunawu suwalemba ntchito nsanga. Nkhaniyi inayamba mu February chaka chino pomwe unduna wa zaumoyo unatulutsa maina a ogwira ntchito zaumoyo omwe boma linawalemba ntchito m’magulu osiyanasiyana. […]

The post Ogwira ntchito zaumoyo awopsyezaso kutengera unduna ku khothi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください